Oweruza 14:18 BL92

18 Ndipo amuna a pamudzi anati kwa Samsoni tsiku lacisanu ndi ciwiri, lisanalowe dzuwa, Cozuna coposa uci nciani; ndi camphamvu coposa mkango nciani? Pamenepo ananena nao,Mukadapanda kulima ndimthandi wanga,Simukadakumika mwambi wanga.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 14

Onani Oweruza 14:18 nkhani