Oweruza 14:19 BL92

19 Ndipo mzimu wa Yehova unamgwera Samsoni, natsikira iye kwa Asikeloni, nawakantha amuna makumi atatu, natenga zobvala zao, nawapatsa okumika mwambiwo zobvala zosinthanitsa. Koma adapsa mtima, nakwera kumka ku nyumba ya atate wace.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 14

Onani Oweruza 14:19 nkhani