Oweruza 14:6 BL92

6 Ndipo unamgwera iye kolimba mzimu wa Yehova, naung'amba monga akadang'amba mwana wa mbuzi, wopandakanthu m'dzanjaliace; koma sanauza atate wace kapena amai wace cimene adacicita.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 14

Onani Oweruza 14:6 nkhani