Oweruza 14:5 BL92

5 Pamenepo anatsikira Samsoni, ndi atate wace ndi mai wace ku Timna, nadza ku minda yamphesa ya Timna; ndipo taona, mwana wa mkango wakomana naye namdzumira.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 14

Onani Oweruza 14:5 nkhani