Oweruza 15:14 BL92

14 Pamene anafika ku Leki Afilisti anapfuula pokomana naye; koma mzimu wa Yehova unamgwera kolimba, ndi zingwe zokhala pa manja ace zinanga bwazi lopserera ndi moto, ndi zomangira zace zinanyotsoka pa manja ace.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 15

Onani Oweruza 15:14 nkhani