Oweruza 15:15 BL92

15 Ndipo anapeza cibwano catsopano ca buru, natambasula dzanja lace nacigwira, nakantha naco amuna cikwi cimodzi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 15

Onani Oweruza 15:15 nkhani