Oweruza 16:17 BL92

17 Pomwepo anamfotokozera mtima wace wonse, nanena naye, Pamutu panga sipanapite lumo, pakuti ndine Mnaziri wa Mulungu ciyambire mimba ya mai wanga; akandimeta, mphamvu yanga idzandicokera, ndidzakhala wofoka wakunga munthu wina ali yense.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 16

Onani Oweruza 16:17 nkhani