Oweruza 16:2 BL92

2 Koma wina anauza a ku Gala, ndi kuti, Samsoni walowa kuno. Pamenepo anamzinga, namlalira usiku wonse pa cipata ca mudzi, nakhala cete usiku wonse ndi kuti, Tidikire mpaka kuca, pamenepo tidzamupha,

Werengani mutu wathunthu Oweruza 16

Onani Oweruza 16:2 nkhani