Oweruza 16:3 BL92

3 Koma Samsoni anagona mpaka pakati pa usiku, nauka pakati pa usiku, nagwira zitseko za pa cipata ca mudzi, ndi mphuthu ziwirizo, nazicotsa ndi mpiringidzo womwe, naziika pa mapewa ace, nakwera nazo pamwamba pa phiri liri pandunji pa Hebroni.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 16

Onani Oweruza 16:3 nkhani