21 Pamenepo Afilisti anamgwira, namkolowola maso, natsika naye ku Gaza, nammanga ndi maunyolo amkuwa; namperetsa m'kaidi.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 16
Onani Oweruza 16:21 nkhani