20 Ndipo anati, Afilisti akugwera, Samsoni. Nagalamuka iye m'tulo tace, nati, Ndizituruka ngati nthawi zina, ndi kudzitakasika. Koma sanadziwa kuti Yehova adamcokera.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 16
Onani Oweruza 16:20 nkhani