Oweruza 16:19 BL92

19 Pamenepo anamgonetsa pa mabondo ace, naitana munthu, nameta njombi zace zisanu ndi ziwiri; nayamba kumzunza, nimcokera mphamvu yaceo

Werengani mutu wathunthu Oweruza 16

Onani Oweruza 16:19 nkhani