Oweruza 16:28 BL92

28 Pamenepo Samsoni anaitana kwa Yehova, nati, Yehova, Mulungu, dikupempha mundikumbukile, ndikupemphani, ndi kundilimbitsa, ndikupemphani, nthawi yino yokha, Mulungu, kuti ndidzilipsiriretu tsopano apa Afilisti, cifukwa ca maso anga awiri.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 16

Onani Oweruza 16:28 nkhani