Oweruza 16:29 BL92

29 Ndipo Samsoni anagwira mizati iwiri ya pakati imene nyumba inakhazikikapo, natsamirapo wina ndi dzanja lamanja, ndi unzace ndi dzanja lamanzere.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 16

Onani Oweruza 16:29 nkhani