Oweruza 17:4 BL92

4 Ndipo pamene anambwezera mai wace ndaramazo, mai wace anatapako ndarama mazana awiri, nazipereka kwa woyenga, ndiye anazipanga fane losema ndi fano loyenga; ndipo linakhala m'nyumba ya Mika.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 17

Onani Oweruza 17:4 nkhani