Oweruza 17:5 BL92

5 Koma munthuyu Mika anali nayo nyumba ya milungu, napanga cobvala ca wansembe, ndi timafano, namninkha zansembe mwana wace wina wamwamuna, amene anakhala wansembe wace.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 17

Onani Oweruza 17:5 nkhani