Oweruza 17:8 BL92

8 Adacokera munthuyo m'mudzi m'Betelehemu-Yuda, kugonera pali ponse akapeza pokhala; ndi pa ulendo wace anafika ku mapiri a Efraimu, ku nyumba ya Mika.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 17

Onani Oweruza 17:8 nkhani