Oweruza 18:18 BL92

18 Atalowa iwo m'nyumba ya Mika, natengako fane losema, cobvala ca wansembe, ndi timafano, ndi fano loyenga, wansembeyo ananena nao, Mucitanji?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 18

Onani Oweruza 18:18 nkhani