Oweruza 18:19 BL92

19 Ndipo ananena naye, Khala cete, tseka pakamwa pako, numuke nafe, nutikhalire atate ndi wansembe wathu; cikukomera nciti, kukhala wansembe wa nyumba ya munthu mmodzi, kapena kukhala wansembe wa pfuko ndi banja m'Israyeli?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 18

Onani Oweruza 18:19 nkhani