Oweruza 18:24 BL92

24 Nati iye, Mwanditengera milungu yanga ndinaipanga, ndi wansembe, ndi kucoka; cinditsaliranso ciani? ndipo muneneranji kwa ine, Cakusowa nciani?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 18

Onani Oweruza 18:24 nkhani