Oweruza 18:25 BL92

25 Koma ana a Dani anati kwa iye, Mau ako asamveke ndi ife, angakugwere anthu owawa mtima, nukataya moyo wako ndi wa iwo a m'nyumba mwako.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 18

Onani Oweruza 18:25 nkhani