Oweruza 18:3 BL92

3 Pokhala iwo m'nyumba ya Mika, anazindikira mau a mnyamata Mleviyo, napambukirako, nanena naye, Anadza nawe kuno ndani? ucitanji muno? ukhala naco ciani kuno?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 18

Onani Oweruza 18:3 nkhani