4 Ndipo ananena nao, Mika anandicitira cakuti cakuti, napangana nane za nchito, ndipo ndikhala wansembe wace.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 18
Onani Oweruza 18:4 nkhani