Oweruza 19:10 BL92

10 Koma munthuyo anakana kugonako usiku, nanyamuka, nacoka, nadza pandunji pa Yebusi (ndiwo Yerusalemu); ndi pamodzi naye panali aburu awiri omangirira mbereko; anali nayenso mkazi wace wamng'ono.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:10 nkhani