Oweruza 19:11 BL92

11 Pofika iwo pa Yebusi linalimkulowa dzuwa, ndi mnyamata anati kwa mbuye wace, Tiyeni, tipambukire mudzi uwu wa Ayebusi ndi kugona pomwepa.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:11 nkhani