Oweruza 19:2 BL92

2 Koma mkazi wace wamng'ono anacita cigololo akali naye, namcokera kumka ku nyumba ya atate wace ku Betelehemu-Yuda, nakhalako nthawi ya miyezi inai.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:2 nkhani