Oweruza 19:3 BL92

3 Koma anauka mwamuna wace namtsata kukamba naye zamtima, kumbwezanso; napita ndi mnyamata wace, ndi aburu awiri. Ndipo mkaziyo anadza naye ku nyumba ya atate wace. Ndipo pakumuona atate wa mkaziyo, anakondwera kukomana naye.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:3 nkhani