Oweruza 19:4 BL92

4 Ndipo mpongozi wace, ndiye atate wa mkaziyo, anamuimika kuti akhale naye masiku atatu; nadya namwa nagona komweko.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:4 nkhani