Oweruza 19:5 BL92

5 Ndipo kunali, tsiku lacinai, analawirira mamawa, nanyamuka iye kucoka; koma atate wa mkaziyo anati kwa mkamwini wace, Limbitsa mtima wako ndi mkate pang'ono, ndipo utatero upite.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:5 nkhani