Oweruza 19:6 BL92

6 Nakhala pansi nadya namwa onse awiri pamodzi; nati kwa munthuyo atate wa mkaziyo, Ubvomere, ugone kuno usiku, nusekerere mtima wako.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:6 nkhani