Oweruza 19:23 BL92

23 Ndipo munthu mwini nyumba anawaturukira nanena nao, lai, abale anga, musacite coipa cotere; popeza mwamuna uyu walowa m'nyumba mwanga, musacite copusa ici.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:23 nkhani