Oweruza 19:24 BL92

24 Taonani, mwana wanga wamkazi ndiye namwali, ndi mkazi wace wamng'onoyo siwa; ndiwaturutse iwo, muwacepetse iwo, ndi kuwacitira monga muyesa cokoma; koma mwamuna uyu musamcitire copusa ici.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:24 nkhani