Oweruza 20:1 BL92

1 Pamenepo anaturuka ana onse a Israyeli, nuunjikana msonkhano kwa Yehova ku Mizipa ngati munthu mmodzi, kuyambira ku Dani mpaka Beereseba ndi dziko la Gileadi lomwe.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:1 nkhani