Oweruza 19:30 BL92

30 Ndipo kunali kuti onse amene anaciona anati, Sicinacitika, inde sicinaoneka cotere ciyambire tsiku lokwera ana a Israyeli kuturuka m'dziko la Aigupto mpaka lero lino; lingiriranipo, mupangane nzeru, nimunene.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:30 nkhani