Oweruza 19:29 BL92

29 Ndipo pofika iye kunyumba kwace, anatenga mpeni, nagwira mkazi wace wamng'onoyo namgawa ciwalo ciwalo magawo khumi ndi awiri, namtumiza ku mame onse a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:29 nkhani