Oweruza 20:14 BL92

14 Ndipo ana a Benjamini anasonkhana kucokera ku midzi kumka ku Gibeya, kuti aturuke kulimbana ndi ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:14 nkhani