Oweruza 20:15 BL92

15 Ndipo anawerenga ana a Benjamini a m'midzi tsiku lija amuna zikwi makumi awiri mphambu zisanu ndi cimodzi akusolola lupanga; osawerenga okhala m'Gibeya, ndiwo amuna osankhika mazana asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:15 nkhani