Oweruza 20:18 BL92

18 Nauka ana a Israyeli, nakwera kumka ku Beteli, nafunsira kwa Mulungu, nati, Ayambe ndani kutikwerera pa ana a Benjamini? Ndipo Yehova anati, Ayambe ndi Yuda.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:18 nkhani