Oweruza 20:35 BL92

35 Ndipo Yehova anakantha Benjamini pamaso pa Israyeli; ndi ana a Israyeli anawaononga a Benjamini tsiku lija amuna zikwi makumi awiri ndi zisanu, kudza zana limodzi; awa onse ndiwo akusolola lupanga.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:35 nkhani