Oweruza 20:36 BL92

36 Ndipo ana a Benjamini anaona kuti takanthidwa; popeza amuna a Israyeli anawapatsa Abenjamini malo, pakuti anatama olalira amene anawaikiratu pa Gibeya.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:36 nkhani