Oweruza 20:40 BL92

40 Koma pamene mtambo unayamba kukwera m'mudzi ngati utsi uti tolo, Abenjamini anaceuka, ndipo taonani, pamodzi ponse panafuka utsi kumwamba.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:40 nkhani