Oweruza 20:39 BL92

39 Ndi nkhondo ya Israyeli inathawa, ndipo Benjamini anayamba kuwakantha ndi kuwagwaza amuna a Israyeli, ngati amuna makumi atatu, pakuti anati, Ndithu Tawakantha konse pamaso pathu, monga ku nkhondo yoyambayo.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:39 nkhani