38 Koma kunali cizindikilo coikika pakati pa amuna a Israyeli ndi olalirawo, ndico cakuti afukitse mtambo wa utsi kumudzi.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 20
Onani Oweruza 20:38 nkhani