Oweruza 21:21 BL92

21 nimuyang'ane, ndipo taonani, ataturuka ana akazi a Silo kubvinabvina, pamenepo muturuke m'minda yamphesa ndi kudzigwirira yense mkazi wace mwa ana akazi a Silo, ndi kumuka naye ku dziko la Benjamini.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 21

Onani Oweruza 21:21 nkhani