Oweruza 21:22 BL92

22 Ndipo kudzali, akatifikira atate ao kapena alongo ao kunena nafe mlandu, tidzanena nao, Mutipatse awa, pakuti sitinawatengera yense mkazi wace kunkhondo; pakuti inunso simunawaninkha awa; mukadatero mukadaparamula tsopano.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 21

Onani Oweruza 21:22 nkhani