23 Nacita cotere ana a Benjamini, nadzitengera akazi monga mwa kuwerenga kwao, a obvina aja, amene anawatenga mwacifwamba; namuka iwo nabwerera ku colowa cao, namanga midzi, nakhalamo.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 21
Onani Oweruza 21:23 nkhani