24 Ndipo ana a Israyeli anacokako nthawi ija yense kumka ku pfuko lace, ndi banja lace, naturukako yense kumka ku colowa cace.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 21
Onani Oweruza 21:24 nkhani