5 Ndipo anakhala patsinde pa mgwalangwa wa Debora pakati pa Rama ndi Beteli ku mapiri a Efraimu; ndi ana a Israyeli anakwera kwa iye awaweruze.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 4
Onani Oweruza 4:5 nkhani