19 Anadza mafumu, nathira nkhondoPamen'epo anathira nkhondo mafumu a Kanani.M'Taanaki, ku madzi a Megido;Osatengako phindu la ndarama.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 5
Onani Oweruza 5:19 nkhani