3 Imvani mafumu inu; cherani makutu, akalonga inu;Ndidzayimbira ine Yehova, inetu;Ndidzamuyimbira nyimbo, Yehova, Mulungu wa Israyeli,
Werengani mutu wathunthu Oweruza 5
Onani Oweruza 5:3 nkhani